Afilipi 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ine, ndikuyembekeza kuti Ambuye Yesu andilola kutumiza Timoteyo+ kwa inu posachedwapa kuti ndidzalimbikitsidwe ndikadzamva mmene zinthu zilili kwa inu. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,9/15/1999, tsa. 30
19 Koma ine, ndikuyembekeza kuti Ambuye Yesu andilola kutumiza Timoteyo+ kwa inu posachedwapa kuti ndidzalimbikitsidwe ndikadzamva mmene zinthu zilili kwa inu.