Afilipi 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye adzasintha thupi lathu lonyozekali kuti lifanane* ndi thupi lake laulemerero.+ Adzachita zimenezi pogwiritsa ntchito mphamvu zake zazikulu zimene zimamuthandiza kugonjetsa zinthu zonse kuti zikhale pansi pake.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:21 Kukambitsirana, tsa. 109
21 Iye adzasintha thupi lathu lonyozekali kuti lifanane* ndi thupi lake laulemerero.+ Adzachita zimenezi pogwiritsa ntchito mphamvu zake zazikulu zimene zimamuthandiza kugonjetsa zinthu zonse kuti zikhale pansi pake.+