3 Ife amene tasonyeza chikhulupiriro tikulowadi mumpumulowo. Ponena za mpumulo umenewu iye anati: “Choncho ndinalumbira nditakwiya kuti, ‘Sadzalowa mumpumulo wanga,’”+ ngakhale kuti anali atamaliza ntchito zake pa nthawi imene dziko linkakhazikitsidwa.+