Aheberi 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 patapita nthawi, Mulungu ananena mu salimo la Davide, ngati mmene tanenera kale mu kalatayi kuti: “Lero anthu inu mukamva mawu a Mulungu, musaumitse mitima yanu.”+ Choncho wapatula tsiku limene akulitchula kuti “Lero.” Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, tsa. 17-18
7 patapita nthawi, Mulungu ananena mu salimo la Davide, ngati mmene tanenera kale mu kalatayi kuti: “Lero anthu inu mukamva mawu a Mulungu, musaumitse mitima yanu.”+ Choncho wapatula tsiku limene akulitchula kuti “Lero.”