Aheberi 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tikufuna kuti nonsenu mupitirize kusonyeza khama limene munali nalo poyamba, kuti chiyembekezo chanu chikhale chotsimikizika+ mpaka mapeto.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:11 Nsanja ya Olonda,1/1/2006, tsa. 242/1/2004, tsa. 30
11 Koma tikufuna kuti nonsenu mupitirize kusonyeza khama limene munali nalo poyamba, kuti chiyembekezo chanu chikhale chotsimikizika+ mpaka mapeto.+