Aheberi 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anachita zimenezo kuti pa zinthu ziwiri zosasinthika, zomwe chifukwa cha zimenezi nʼzosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe nʼkumakhulupirira kwambiri* zinthu zimene tikuyembekezera. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:18 Nsanja ya Olonda,1/15/1986, tsa. 18
18 Anachita zimenezo kuti pa zinthu ziwiri zosasinthika, zomwe chifukwa cha zimenezi nʼzosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe nʼkumakhulupirira kwambiri* zinthu zimene tikuyembekezera.