1 Yohane 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano. Koma ndikukulemberani lamulo lakale limene mwakhala nalo kuyambira pachiyambi.+ Lamulo lakaleli ndi mawu amene munawamva. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Nsanja ya Olonda,9/15/2013, tsa. 108/1/2011, ptsa. 29-3012/15/2008, tsa. 271/15/1987, tsa. 28
7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano. Koma ndikukulemberani lamulo lakale limene mwakhala nalo kuyambira pachiyambi.+ Lamulo lakaleli ndi mawu amene munawamva.