Yuda 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu amenewa amakonda kungʼungʼudza,+ kudandaula za moyo wawo, amangochita zimene amalakalaka+ komanso amalankhula modzitama. Amatamandanso anthu nʼcholinga choti apezepo phindu.+
16 Anthu amenewa amakonda kungʼungʼudza,+ kudandaula za moyo wawo, amangochita zimene amalakalaka+ komanso amalankhula modzitama. Amatamandanso anthu nʼcholinga choti apezepo phindu.+