Genesis 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma pakufunika chinthu chimodzi kuti anthuwa alole kukhala nafe limodzi n’kukhala anthu amodzi ndi ife. Akuti adzatero pokhapokha mwamuna aliyense pakati pathu atadulidwa+ ngati mmene iwonso alili.
22 Koma pakufunika chinthu chimodzi kuti anthuwa alole kukhala nafe limodzi n’kukhala anthu amodzi ndi ife. Akuti adzatero pokhapokha mwamuna aliyense pakati pathu atadulidwa+ ngati mmene iwonso alili.