Genesis 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pa tsiku lachitatu, pamene anthuwo anali pa ululu,+ ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi,+ alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake n’kukalowa mumzindawo mosaonetsera cholinga chawo. Kenako anayamba kupha mwamuna aliyense.+
25 Koma pa tsiku lachitatu, pamene anthuwo anali pa ululu,+ ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi,+ alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake n’kukalowa mumzindawo mosaonetsera cholinga chawo. Kenako anayamba kupha mwamuna aliyense.+