Genesis 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu anamuuza kuti: “Iwe dzina lako ndi Yakobo.+ Koma kuyambira tsopano, dzina lako silikhalanso Yakobo, ukhala Isiraeli.” Choncho anayamba kumutchula kuti Isiraeli.+
10 Mulungu anamuuza kuti: “Iwe dzina lako ndi Yakobo.+ Koma kuyambira tsopano, dzina lako silikhalanso Yakobo, ukhala Isiraeli.” Choncho anayamba kumutchula kuti Isiraeli.+