Genesis 38:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamene anali kum’tulutsa, Tamarayo anatumiza mawu kwa apongozi ake kuti: “Mwiniwake zinthu izi ndiye anandipatsa pakatipa.”+ Ananenanso kuti: “Chonde ziyang’anitsitseni,+ muone kuti mpheteyo ndi chingwe chake, komanso ndodoyo n’zandani.”+
25 Pamene anali kum’tulutsa, Tamarayo anatumiza mawu kwa apongozi ake kuti: “Mwiniwake zinthu izi ndiye anandipatsa pakatipa.”+ Ananenanso kuti: “Chonde ziyang’anitsitseni,+ muone kuti mpheteyo ndi chingwe chake, komanso ndodoyo n’zandani.”+