Genesis 41:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma Farao anagonanso n’kulota maloto ena. M’malotowa anaona ngala za tirigu 7 zikutuluka paphesi limodzi. Ngalazo zinali zokhwima ndi zazikulu bwino.+
5 Koma Farao anagonanso n’kulota maloto ena. M’malotowa anaona ngala za tirigu 7 zikutuluka paphesi limodzi. Ngalazo zinali zokhwima ndi zazikulu bwino.+