Genesis 46:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Onse a m’nyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:27 Nsanja ya Olonda,9/15/2002, tsa. 275/1/1987, ptsa. 19-20
27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Onse a m’nyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+