-
Genesis 49:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Adzaona kuti malo opumirawo ndi abwino, ndi kuti dzikolo n’losangalatsa. Adzaweramitsa phewa lake kuti anyamule akatundu, ndipo adzakakamizidwa kugwira ntchito yakalavulagaga ngati kapolo.
-