Genesis 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Abulamu anauza mfumu ya ku Sodomuyo kuti: “Ndikukweza manja anga kulumbira+ kwa Yehova Mulungu Wam’mwambamwamba, Amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.
22 Koma Abulamu anauza mfumu ya ku Sodomuyo kuti: “Ndikukweza manja anga kulumbira+ kwa Yehova Mulungu Wam’mwambamwamba, Amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.