Genesis 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu m’masomphenya,+ kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:1 Nsanja ya Olonda,4/15/2010, tsa. 8
15 Ndiyeno zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu m’masomphenya,+ kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+