Genesis 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngelo wa Yehovayo anauza Hagara kuti: “Bwerera kwa mbuye wako ndipo ukadzichepetse kwa iye.”+