Genesis 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwamukomera kale mtima mtumiki wanu,+ ndipo mwaonetsa kukoma mtima kwanu kosatha+ kuti mupulumutse moyo wanga.+ Koma chonde, sinditha kuthawira kudera la kumapiri chifukwa tsoka lingakandipeze kumeneko, ndipo ndingakafe ndithu.+
19 Mwamukomera kale mtima mtumiki wanu,+ ndipo mwaonetsa kukoma mtima kwanu kosatha+ kuti mupulumutse moyo wanga.+ Koma chonde, sinditha kuthawira kudera la kumapiri chifukwa tsoka lingakandipeze kumeneko, ndipo ndingakafe ndithu.+