Genesis 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mkaziyo atamva zimenezo, anayamba kuona kuti zipatso za mtengowo n’zokoma kudya, zokhumbirika ndi zosiririka.+ Choncho anathyola chipatso cha mtengowo n’kudya. Pambuyo pake, anapatsako mwamuna wake pamene anali limodzi, ndipo nayenso anadya.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 26 Nsanja ya Olonda,9/1/2013, tsa. 155/15/2011, tsa. 1711/15/2000, ptsa. 25-276/15/1990, tsa. 318/1/1989, ptsa. 22-235/1/1986, tsa. 11
6 Mkaziyo atamva zimenezo, anayamba kuona kuti zipatso za mtengowo n’zokoma kudya, zokhumbirika ndi zosiririka.+ Choncho anathyola chipatso cha mtengowo n’kudya. Pambuyo pake, anapatsako mwamuna wake pamene anali limodzi, ndipo nayenso anadya.+
3:6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 26 Nsanja ya Olonda,9/1/2013, tsa. 155/15/2011, tsa. 1711/15/2000, ptsa. 25-276/15/1990, tsa. 318/1/1989, ptsa. 22-235/1/1986, tsa. 11