Genesis 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova Mulungu atamva zimenezi, anafunsa mkaziyo kuti: “Ndiye chiyani wachitachi?” Mkaziyo anayankha kuti: “Njoka ndi imene inandinyenga, ndipo ine ndadya.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Galamukani!,9/8/1998, tsa. 30 Nsanja ya Olonda,8/1/1989, ptsa. 22-232/15/1987, tsa. 12
13 Yehova Mulungu atamva zimenezi, anafunsa mkaziyo kuti: “Ndiye chiyani wachitachi?” Mkaziyo anayankha kuti: “Njoka ndi imene inandinyenga, ndipo ine ndadya.”+