Genesis 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Yakobo anati: “Choyamba lumbira kwa ine!”+ Ndipo iye analumbiradi kwa Yakobo, n’kugulitsa kwa iye ukulu wake monga woyamba kubadwa.+
33 Ndiyeno Yakobo anati: “Choyamba lumbira kwa ine!”+ Ndipo iye analumbiradi kwa Yakobo, n’kugulitsa kwa iye ukulu wake monga woyamba kubadwa.+