Genesis 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anachita mantha n’kunenanso kuti:+ “Malo ano ndi oopsa!+ Ndithu malo ano ndi nyumba ya Mulungu,+ ndiponso ndi khomo la kumwamba.”
17 Iye anachita mantha n’kunenanso kuti:+ “Malo ano ndi oopsa!+ Ndithu malo ano ndi nyumba ya Mulungu,+ ndiponso ndi khomo la kumwamba.”