Genesis 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Yakobo anauza Labani kuti: “Ndipatseni mkazi wanga, chifukwa masiku anga akwana, kuti ndim’kwatire.”*+
21 Kenako Yakobo anauza Labani kuti: “Ndipatseni mkazi wanga, chifukwa masiku anga akwana, kuti ndim’kwatire.”*+