Genesis 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene ziweto zinali m’nthawi yotentha thupi kukonzekera kutenga bere, ndinakweza maso anga n’kuona m’maloto+ mbuzi zamphongo zikukwera zazikazi. Mbuzi zamphongozo zinali zamizeremizere, zamawangamawanga ndi zamathothomathotho.+
10 Pamene ziweto zinali m’nthawi yotentha thupi kukonzekera kutenga bere, ndinakweza maso anga n’kuona m’maloto+ mbuzi zamphongo zikukwera zazikazi. Mbuzi zamphongozo zinali zamizeremizere, zamawangamawanga ndi zamathothomathotho.+