Genesis 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Labani anafunsa Yakobo kuti: “Ndiye chiyani wachitachi, kuchoka mondizembera, n’kutenga ana anga aakazi ngati akapolo ogwidwa kunkhondo?+
26 Ndiyeno Labani anafunsa Yakobo kuti: “Ndiye chiyani wachitachi, kuchoka mondizembera, n’kutenga ana anga aakazi ngati akapolo ogwidwa kunkhondo?+