Genesis 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikanatha kukuchitani choipa anthu inu,+ koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.’+
29 Ndikanatha kukuchitani choipa anthu inu,+ koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.’+