Genesis 31:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pa zaka 20 zonsezi zimene ndakhala nanu, nkhosa zanu zazikazi ndi mbuzi zanu zazikazi sizinaberekepo mwana wakufa.+ Ndiponso, chikhalire sindinadyeko ndi imodzi yomwe ya nkhosa zanu zamphongo.
38 Pa zaka 20 zonsezi zimene ndakhala nanu, nkhosa zanu zazikazi ndi mbuzi zanu zazikazi sizinaberekepo mwana wakufa.+ Ndiponso, chikhalire sindinadyeko ndi imodzi yomwe ya nkhosa zanu zamphongo.