Ekisodo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu+ kukachingamira Mose.” Chotero Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ nam’psompsona.
27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu+ kukachingamira Mose.” Chotero Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ nam’psompsona.