-
Ekisodo 7:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Aliyense wa iwo anaponya pansi ndodo yake, ndipo zinasanduka njoka zazikulu. Koma ndodo ya Aroni inameza ndodo zawo.
-