Ekisodo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+
22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+