19 Musamadzapezeke mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa m’nyumba zanu kwa masiku 7, chifukwa aliyense wakudya mtanda wokhala ndi chofufumitsa, kaya ndi mlendo kapena mbadwa ya Isiraeli,+ munthu ameneyo adzaphedwa kuti asakhalenso mu khamu la Isiraeli.+