Ekisodo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero Mose anauza Yoswa* kuti:+ “Tisankhire amuna, ndipo upite nawo+ kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona m’dzanja langa.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:9 Nsanja ya Olonda,12/1/2002, ptsa. 9-10
9 Zitatero Mose anauza Yoswa* kuti:+ “Tisankhire amuna, ndipo upite nawo+ kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona m’dzanja langa.”+