Ekisodo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo anthuwo uwadulire malire kuzungulira phiri lonse, ndi kuwauza kuti, ‘Onetsetsani kuti musakwere m’phiri, ndipo musakhudze tsinde lake. Aliyense amene adzakhudza phirili adzaphedwa ndithu.+
12 Ndipo anthuwo uwadulire malire kuzungulira phiri lonse, ndi kuwauza kuti, ‘Onetsetsani kuti musakwere m’phiri, ndipo musakhudze tsinde lake. Aliyense amene adzakhudza phirili adzaphedwa ndithu.+