Ekisodo 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Munthu akagulitsa mwana wake wamkazi kukhala kapolo,+ sadzachoka mmene akapolo aamuna amachokera.