Ekisodo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati mbuye wake sanakondwere naye kuti akhale mkazi wake wamng’ono+ koma wamulola kuwomboledwa, mbuyeyo alibe ufulu womugulitsa kwa anthu a mtundu wina chifukwa wam’chitira zachinyengo.
8 Ngati mbuye wake sanakondwere naye kuti akhale mkazi wake wamng’ono+ koma wamulola kuwomboledwa, mbuyeyo alibe ufulu womugulitsa kwa anthu a mtundu wina chifukwa wam’chitira zachinyengo.