Ekisodo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Munthu akapatsa mnzake ndalama kapena katundu wina kuti amusungire,+ zinthuzo n’kubedwa m’nyumba ya mnzakeyo, wakubayo akapezeka azilipira zowirikiza kawiri.+
7 “Munthu akapatsa mnzake ndalama kapena katundu wina kuti amusungire,+ zinthuzo n’kubedwa m’nyumba ya mnzakeyo, wakubayo akapezeka azilipira zowirikiza kawiri.+