Ekisodo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Koma ngati munthu wabwereka chiweto kwa mnzake+ ndipo chalumala kapena chafa mwiniwake palibe, wobwerekayo azilipira ndithu.+
14 “Koma ngati munthu wabwereka chiweto kwa mnzake+ ndipo chalumala kapena chafa mwiniwake palibe, wobwerekayo azilipira ndithu.+