Ekisodo 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno upange ngowe 50 zamkuwa+ ndi kuzilowetsa m’zingwe zopota zokolekamo ngowezo, n’kulumikiza nsaluzo kuti zikhale chinsalu chimodzi cha chihema.+
11 Ndiyeno upange ngowe 50 zamkuwa+ ndi kuzilowetsa m’zingwe zopota zokolekamo ngowezo, n’kulumikiza nsaluzo kuti zikhale chinsalu chimodzi cha chihema.+