Ekisodo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Upangenso mphete ziwiri zagolide ndi kuziika pansalu ziwiri za pamapewa za efodi m’munsi mwake, kutsogolo kwa nsaluzo, pafupi ndi polumikizira, pamwamba pa lamba wa efodi.+
27 Upangenso mphete ziwiri zagolide ndi kuziika pansalu ziwiri za pamapewa za efodi m’munsi mwake, kutsogolo kwa nsaluzo, pafupi ndi polumikizira, pamwamba pa lamba wa efodi.+