Ekisodo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mumpendero wake wa m’munsi upangemo makangaza* a ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi ulusi wofiira kwambiri kuzungulira mpenderowo. Upangenso mabelu+ agolide pakati pa makangazawo kuzungulira mpenderowo.
33 Mumpendero wake wa m’munsi upangemo makangaza* a ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi ulusi wofiira kwambiri kuzungulira mpenderowo. Upangenso mabelu+ agolide pakati pa makangazawo kuzungulira mpenderowo.