Ekisodo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Mose anauza Yehova kuti: “Inu mukundiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa,’ koma simunandidziwitse amene mudzam’tuma kuti ndiyende naye limodzi. Komanso mwanena kuti ‘Ndikukudziwa bwino, ndi dzina lako lomwe,+ ndipo ndakukomera mtima.’
12 Tsopano Mose anauza Yehova kuti: “Inu mukundiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa,’ koma simunandidziwitse amene mudzam’tuma kuti ndiyende naye limodzi. Komanso mwanena kuti ‘Ndikukudziwa bwino, ndi dzina lako lomwe,+ ndipo ndakukomera mtima.’