Ekisodo 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Mose anatsika m’phiri la Sinai atanyamula miyala iwiri ija ya Umboni m’manja mwake,+ koma iye sanadziwe kuti nkhope yake inali kuwala chifukwa anali atalankhula ndi Mulungu.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:29 Nsanja ya Olonda,7/15/1990, ptsa. 15-163/15/1990, tsa. 7
29 Ndiyeno Mose anatsika m’phiri la Sinai atanyamula miyala iwiri ija ya Umboni m’manja mwake,+ koma iye sanadziwe kuti nkhope yake inali kuwala chifukwa anali atalankhula ndi Mulungu.+