Ekisodo 39:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndipo Mose ataona ntchito yonse, anaona kuti achita zonse monga mmene Yehova analamulira. Iwo anachitadi momwemo. Pamenepo Mose anawadalitsa.+
43 Ndipo Mose ataona ntchito yonse, anaona kuti achita zonse monga mmene Yehova analamulira. Iwo anachitadi momwemo. Pamenepo Mose anawadalitsa.+