17 Ndiyeno aziing’amba pakati cham’mapiko mwake, koma osailekanitsa.+ Kenako wansembe aziitentha paguwa lansembe pamwamba pa nkhuni zimene zili pamoto. Imeneyi ndi nsembe yopsereza,+ nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+