Levitiko 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngati akupereka nkhosa yaing’ono yamphongo monga nsembe yake, aziipereka kwa Yehova.+