20 “Aroni ndi ana ake apereke nsembe+ iyi kwa Yehova monga nsembe yambewu: ufa wosalala+ wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa.+ Hafu imodzi m’mawa ndipo hafu inayo madzulo. Aliyense wa iwo azichita zimenezi nthawi zonse pa tsiku la kudzozedwa kwake.+