Levitiko 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anapereka nsembe yambewu.+ Anatapako nsembeyo kudzaza dzanja lake ndi kuitentha paguwa lansembe, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya m’mawa.+
17 Kenako anapereka nsembe yambewu.+ Anatapako nsembeyo kudzaza dzanja lake ndi kuitentha paguwa lansembe, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya m’mawa.+