Levitiko 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mudye nsembeyo m’malo oyera,+ chifukwa ndi gawo lanu komanso ndi gawo la ana anu kuchokera pa nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Zimenezi n’zimene ndalamulidwa.
13 Mudye nsembeyo m’malo oyera,+ chifukwa ndi gawo lanu komanso ndi gawo la ana anu kuchokera pa nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Zimenezi n’zimene ndalamulidwa.