Levitiko 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Akatero, aziika zofukizazo pamoto umene uli pamaso pa Yehova,+ ndipo utsi wa zofukizazo uzikuta chivundikiro cha Likasa,+ chimene chili pa Umboni,+ kuopera kuti angafe. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:13 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2019, ptsa. 20-22 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 87
13 Akatero, aziika zofukizazo pamoto umene uli pamaso pa Yehova,+ ndipo utsi wa zofukizazo uzikuta chivundikiro cha Likasa,+ chimene chili pa Umboni,+ kuopera kuti angafe.